CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YEREMIYA 35-38
Ebedi-meleki—Citsanzo ca Kulimba Mtima na Kukoma Mtima
Ebedi-meleki, nduna ya m’bwalo la Mfumu Zedekiya, anaonetsa makhalidwe aumulungu
38:7-13
Anacita zinthu molimba mtima ndi mwacangu mwa kukalankhula ndi Mfumu Zedekiya ndi kutulutsa Yeremiya m’citsime
Anaonetsanso kukoma mtima mwa kupatsa Yeremiya tuzidutswa twa nsalu kuti aike m’khwapa mwake kuti nthambo zisamuvulaze