LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 December tsa. 3
  • “Adzagwila Covala ca Munthu Amene ndi Myuda”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Adzagwila Covala ca Munthu Amene ndi Myuda”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Nkhani Zofanana
  • Tipita Nanu Limodzi
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
  • “Tipita Nanu Limodzi”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
  • “Ana Anu Aamuna ndi Ana Anu Aakazi Adzanenela”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Amabala Zipatso Ngakhale ni Okalamba
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 December tsa. 3
Mwamuna wagwila covala ca Myuda

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | ZEKARIYA 1-8

“Adzagwila Covala ca Munthu Amene ndi Myuda”

8:20-23

Amuna 10 ocokela m’zinenelo zonse za anthu adzagwila covala ca Myuda, na kukamba kuti, “anthu inu tipita nanu limodzi.” M’masiku ano otsiliza, anthu ocokela m’mitundu yonse akukhamukila kwa Yehova kuti amulambile pamodzi na Akhristu odzozedwa

Kodi a nkhosa zina masiku ano amathandizila odzozedwa m’njila ziti?

  • A Mboni za Yehova aŵili akulalikila

    Amagwila nchito yolalikila na mtima wonse

  • Aponya ndalama m’bokosi la zopeleka

    Amacita zopeleka mopanda kaso pothandizila nchitoyi

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani