Woyang’anila dela na mkazi wake ali pa nchito yawo ku France, mu 1957
Makambilano Acitsanzo
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi dzina la Mulungu n’ndani?
Lemba: Sal. 83:18
Ulalo: Tidziŵa bwanji kuti Yehova Mulungu afuna tikhale mabwenzi ake?
○●○ KUBWELELAKO KOYAMBA
Funso: Tidziŵa bwanji kuti Yehova Mulungu afuna tikhale mabwenzi ake?
Lemba: Yak. 4:8
Ulalo: Tingacite ciani kuti tikhale mabwenzi a Mulungu?
○○● KUBWELELAKO KACIŴILI
Funso: Tingacite ciani kuti tikhale mabwenzi a Mulungu?
Lemba: Yoh. 17:3
Ulalo: Tingamuyandikile bwanji Mulungu popeza kuti sitimuona?