LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 January tsa. 2
  • “Cifunilo ca Yehova Cicitike”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Cifunilo ca Yehova Cicitike”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Muzionetsa kuti Mumaona Moyo Mmene Yehova Amauonela
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Apatsidwa Mlandu Wakuti ni Wovutitsa Komanso Woukila Boma
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • “Cipulumutso Canu Cikuyandikila”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Paulo Apempha Kukaonekela kwa Kaisara Kenako Alalikila Mfumu Herode Agiripa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 January tsa. 2

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 21-22

“Cifunilo ca Yehova Cicitike”

21:8-14

Paulo anamva kuti mzimu woyela ukumutsogolela kupita ku Yerusalemu kumene anakumana na masautso. (Mac. 20:22, 23) Conco, pamene Akhristu a kumeneko anayamba kumucondelela kuti asapite, iye anayankha kuti: “N’cifukwa ciani mukulila ndi kunditayitsa mtima?” (Mac. 21:13) Sitifunika kufooketsa ena amene akuyesetsa kudzipeleka na mtima wonse potumikila Yehova.

Ngati Mkhristu mzathu wadzipeleka pa zocitika zotsatilazi, kodi tingam’limbikitse bwanji m’malo momufooketsa?

  • M’bale akutsuka mawindo

    Ngati wasankha nchito ya malipilo ocepa, kuti awonjezele utumiki wake, m’malo mwa nchito ya malipilo oculuka

  • Banja likucita ulaliki wapoyela ku dziko lacilendo

    Ngati akufuna kusamuka kuti akatumikile ku mpingo wosoŵa

  • M’bale wosaona na mkazi wake akulalikila

    Ngati amayesetsa kucita zambili mu utumiki ngakhale kuti thanzi lake ni lofooka

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani