LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 11
  • Khalanibe Ofatsa Mukapanikizika na Mayeso

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Khalanibe Ofatsa Mukapanikizika na Mayeso
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Yesetsani Kukhala Ofatsa Kuti Mukondweletse Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Pitilizani Kuonetsa Kukula kwa Cikondi Canu Pa Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Funani Yehova Tsiku la Mkwiyo Wake Lisanafike
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 11
M’bale wacinyamata wanyamuka kuti azipita ku misonkhano. Iye wakhalabe wodekha pamene atate ake amene si Mboni akumukalipila. M’nyumba muli zifanizilo zacipembedzo komanso mtengo wa Khrisimasi.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Khalanibe Ofatsa Mukapanikizika na Mayeso

Kufatsa kwa Mose kunayesedwa pamene Aisiraeli anali kukangana naye komanso pamene anapanikizika maganizo (Num. 20:2-5; w19.02 12 ¶19)

Panthawiyi, Mose analephela kukhala wofatsa (Num. 20:10; w19.02 13 ¶20-21)

Yehova analanga Mose na Aroni cifukwa ca colakwa cacikulu cimene anacita (Num. 20:12; w09 9/1 19 ¶5)

Munthu wofatsa sakwiya msanga, sakhala wodzikuza, kapena wonyada. Ngakhale pamene ena amukhumudwitsa, amapilila moleza mtima, sakwiya, sasunga cakukhosi, kapena kubwezela.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani