LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 7
  • Seŵenzetsani Zida Zofufuzila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Seŵenzetsani Zida Zofufuzila
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Funsani Mafunso
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Afikeni Pamtima Anthu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Landilani Thandizo la Yehova Kupitila M’pemphelo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Seŵenzetsani Mawu a Mulungu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 7

CITANI KHAMA PA ULALIKI | WONJEZELANI CIMWEMWE CANU MU ULALIKI

Seŵenzetsani Zida Zofufuzila

Yehova amatipatsa zida zotithandiza kuphunzitsa mwaluso, monga mavidiyo, mathilakiti, magazini, mabulosha, mabuku, ndiponso cida cathu cacikulu, Baibo. (2 Tim. 3:16) Watipatsanso zida zofufuzila zimene zingatithandize kufotokoza bwino Malemba. Zida zimenezi ni Watchtower Laibulali, JW Laibulali® app, LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower™, komanso Buku Lofufuzila Nkhani la Mboni za Yehova.

Mudzapeza cimwemwe pamene mukufufuza Cuma cauzimu m’zofalitsa zambili zimene tili nazo. Phunzitsani ophunzila Baibo anu kudziŵa mmene angaseŵenzetsele zida zimenezi. Mukatelo, nawonso adzakhala acimwemwe cifukwa adzadzipezela okha mayankho a m’Baibo pa mafunso awo.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI PEZANI CIMWEMWE PA NCHITO YOPANGA OPHUNZILA—LANDILANI THANDIZO LA YEHOVA—ZIDA ZOFUFUZILA. PAMBUYO PAKE, YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Cithunzi coonetsa zocitika za mu vidiyo yakuti “Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Landilani Thandizo la Yehova—Zida Zofufuzila.” Rose akufotokozela Neeta zimene amakhulupilila, zakuti zinthu zinacita kusandulika.

    Kodi Rose anafunsa funso lotani potsutsa mfundo yakuti zinthu zinacita kulengedwa?

  • Cithunzi coonetsa zocitika za mu vidiyo yakuti “Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Landilani Thandizo la Yehova—Zida Zofufuzila.” Neeta akuseŵenzetsa Buku Lofufuzila Nkhani pofufuza zambili zokhudza mfundo yakuti zinthu zinacita kulengedwa.

    Kodi Neeta anapeza kuti mfundo zothandiza pa nkhaniyi?

  • Cithunzi coonetsa zocitika za mu vidiyo yakuti “Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Landilani Thandizo la Yehova—Zida Zofufuzila.” Mokondwela Neeta akufotokozela Rose zimene anapeza pambuyo pofufuza.

    Tikapeza mfundo za coonadi na kuuzako ena, timakondwela

    Kodi Neeta anasankha bwanji mfundo zimene zinam’thandiza kwambili Rose?

  • Kodi kuseŵenzetsa zida zathu zofufuzila kunam’thandiza bwanji Neeta?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani