CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Zimene Tingaphunzile pa Nkhani ya Agibeoni
Agibeoni anacita zinthu mwanzelu (Yos. 9:3-6; it-1 930-931)
Akulu a Isiraeli sanacite zinthu mwanzelu cifukwa sanafunsile kwa Yehova (Yos. 9:14, 15; w11 11/15 8 ¶14)
Agibeoni anatumikila Aisiraeli modzicepetsa (Yos. 9:25-27; w04 10/15 18 ¶14)
Agibeoni anali kugwila nchito zotsika cifukwa anafuna kuti Yehova awayanje. Kodi tingatengele bwanji citsanzo cawo ca kudzicepetsa masiku ano?