LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 8
  • Yehova Anacita Pangano na Davide

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Anacita Pangano na Davide
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Muzidalila Thandizo la Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • ‘Madalitso Onsewa Adzakupeza’
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Zimene Zinathandiza Yobu Kukhalabe Woyela
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Pewani Zinthu Zopanda Pake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 8
Mfumu Davide ali pa windo ya nyumba yacifumu, akuyang’ana kunja.

Davide akusinkhasinkha za pangano limene Yehova anacita naye

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Anacita Pangano na Davide

Yehova analonjeza Davide kuti adzakhazikitsa ufumu m’banja lake (2 Sam. 7:11, 12; w10 4/1 20 ¶3; onani cithunzi ca pacikuto)

Mbali zina za pangano limene Yehova anacita na Davide zinakwanilitsidwa mwa Mesiya (2 Sam. 7:13, 14; Aheb. 1:5; w10 4/1 20 ¶4)

Madalitso amene ufumu wa Mesiya udzabweletsa adzakhala amuyaya (2 Sam. 7:15, 16; Aheb. 1:8; w14 10/15 10 ¶14)

Yesu akuyang’ana pa dziko lapansi ali kumwamba pa mpando wake wacifumu.

Dzuŵa na mwezi zimatikumbutsa kuti ufumu wa Mesiya udzakhalapo kwamuyaya. (Sal. 89:35-37) Mukamaziona, muziganizila za madalitso amene Yehova wakulonjezani pamodzi na banja lanu, amene adzakwanilitsidwa kupitila mu Ufumu Wake.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani