LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsa. 12
  • ‘Madalitso Onsewa Adzakupeza’

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • ‘Madalitso Onsewa Adzakupeza’
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Pewani Zinthu Zopanda Pake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Anacita Pangano na Davide
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Zimene Zinathandiza Yobu Kukhalabe Woyela
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Zimene Tingaphunzile pa Mafanizo a m’Nyimbo Youzilidwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 July tsa. 12
Banja laciisiraeli likuceza mosangalala m’munsi mwa mtengo panja pa nyumba yawo. Nkhosa zikudyela capafupi.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

‘Madalitso Onsewa Adzakupeza’

Anthu amene amamvela mawu a Yehova, amapeza madalitso ambili (Deut. 28:1, 3-6; w10 12/15 19 ¶18)

Madalitso a Yehova amabwela kwa atumiki ake amene amamumvela (Deut. 28:2; w01 9/15 10 ¶2)

Yehova amafuna kuti tizimumvela “mokondwela, ndi mtima wosangalala” (Deut. 28:45-47; w10 9/15 8 ¶4)

Abale na alongo a mitundu yosiyana-siyana akudyela pamodzi cakudya pambuyo pa msonkhano waukulu.

Atumiki omvela a Yehova amasangalala na madalitso ambili palipano, ndipo posacedwa adzalandila madalitso oculuka amene iye analonjeza.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani