LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 12
  • Zimene Tingaphunzilepo pa Zipilala Ziŵili

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zimene Tingaphunzilepo pa Zipilala Ziŵili
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Anagwila Nchito Molimbika Cifukwa Cokonda Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Mmene Mungakhalile na Moyo Wopambana
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Muzilimbikitsa Ena pa Nthawi Zovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 12
Khonde la kacisi lokhala na zipilala zamkuwa mbali zonse ziŵili.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Tingaphunzilepo pa Zipilala Ziŵili

Panamangidwa zipilala ziŵili zikulu-zikulu, ndipo anaziika pakhonde la kacisi (1 Maf. 7:15, 16; w13 12/1 13 ¶3)

Zipilalazo zinapatsidwa maina atanthauzo (1 Maf. 7:21; it-1 348)

Aisiraeli akanadalilabe Yehova, iye akanalimbitsa kacisiyo (1 Maf. 7:21; Sal. 127:1)

N’kutheka kuti Yehova anatithandiza kugonjetsa zopinga zambili kuti tiphunzile coonadi. Koma tiyenela kupitiliza kum’dalila kuti ‘tikhalebe ‘olimba m’cikhulupililo.’—1 Akor. 16:13.

Zithunzi: 1. Mtsikana ali kumsika ndipo walandila kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya kamene mlongo wamupatsa. 2. Mtsikanayo akuganizila za khalidwe lake lokoka fodya pamene akuŵelenga buku lakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya kunyumba. 3. Akubatizika.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi nimaonetsa bwanji kuti nimam’dalila Yehova?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani