LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsa. 12
  • Zimene Adani Athu Amacita Poyesa Kutifooketsa

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zimene Adani Athu Amacita Poyesa Kutifooketsa
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Ife Tili ndi Ambili Kuposa Amene Ali ndi Iwo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kucita Zinthu na Mtima Wonse Kumabweletsa Madalitso Oculuka
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli na Malile
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 November tsa. 12
Rabisake na msilikali aimilila kunja kwa mpanda wa Yerusalemu. Rabisakeyo akulankhula ndipo akuloza anthu a mu Yerusalemu na ndodo yake.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Adani Athu Amacita Poyesa Kutifooketsa

Adani athu amayesa kutifooketsa ponenela mabodza abale otitsogolela (2 Maf. 18:19-21; w05 8/1 11 ¶5)

Amayesa kutisoceletsa mwa kufalitsa mabodza onena za Yehova na gulu lathu (2 Maf. 18:22, 25; w10 7/15 13 ¶3)

Iwo amayesa kutikopa kuti tisamvele Yehova mwa kupanga malonjezo abodza (2 Maf. 18:31, 32; w13 11/15 19 ¶14; yb74 177 ¶1)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ningacite ciyani pali pano kuti nidzakhale wolimba pa nthawi ya cizunzo?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani