LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 13
  • Khalanibe Acimwemwe Ngakhale Pamene Mwakumana na Zolefula

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Khalanibe Acimwemwe Ngakhale Pamene Mwakumana na Zolefula
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mukukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Kulitsani Cikhumbo Canu Cofuna Kucita Cifunilo ca Mulungu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Thandizani Acinyamata Kuti Apambane
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kodi Mumaona Kuti Nchito Yamanja si Yokuyenelelani?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 13

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Khalanibe Acimwemwe Ngakhale Pamene Mwakumana na Zolefula

Davide anali kufunitsitsa kumangila Yehova kacisi wokongola (1 Mbiri 17:1, 2; w06 7/15 19 ¶1)

Yehova anauza Davide kuti sindiye adzamange kacisi (1 Mbiri 17:4)

Davide anaikabe maganizo ake pa utumiki umene Yehova anam’patsa (1 Mbiri 17:7; 18:14)

Zithunzi: 1. M’bale wolefuka ali pa njinga ya olemala ndipo akupuma mothandizidwa na cipangizo ca oxygen. 2. Mwacimwemwe m’baleyo akulalikila munthu amene wabwela pa kasitandi ka ulaliki.

Ngati cifukwa ca msinkhu, thanzi, kapena zovuta zina simungakwanitse kucita utumiki winawake, muyenela kuikabe maganizo anu pa zimene mungakwanitse kucita.—Mac. 18:5; w21.08 22-23 ¶11.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani