LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsa. 4
  • Pewani Kutengela Elifazi Popeleka Citonthozo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pewani Kutengela Elifazi Popeleka Citonthozo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Amakondwela Tikamapemphelela Ena
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Limbikitsani Ena ndi Mau Abwino
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • ‘Kodi Munthu Angakhale Waphindu kwa Mulungu?’
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Samalani na Nkhani Zabodza
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 November tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pewani Kutengela Elifazi Popeleka Citonthozo

Elifazi anauza Yobu kuti anthu sangakwanitse kum’kondweletsa Mulungu (Yobu 15:​14-16; w05 9/15 26 ¶4-5)

Mwa zokamba zake, iye anaonetsa kuti kuvutika kwa Yobu n’cifukwa cakuti anali munthu woipa (Yobu 15:20)

Mawu a Elifazi sanam’tonthoze Yobu ayi (Yobu 16:​1, 2)

Elifazi akulata cala Yobu amene ali na zilonda thupi lonse, ndipo anzake aŵili acinyengo akuona zimenezo.

Zimene Elifazi anauza Yobu zinali bodza lamkunkhuniza. Yehova amayamikila zimene timacita pom’tumikila. (Sal. 149:4) Ngakhale anthu olungama nawonso amakumana na mavuto.—Sal. 34:19.

ZOYENELA KUZISINKHASINKHA: Kodi tingalankhule bwanji ‘molimbikitsa kwa amtima wacisoni’?—1 Ates. 5:14; w15 2/15 9 ¶16.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani