March Umoyo ndi Utumiki Wathu Wacikristu—Kabuku ka Msonkhano March 2016 Maulaliki Acitsanzo March 7-13 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | ESITERE 6-10 Esitere Anaimila Yehova ndi Anthu Ake KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Konzani Ulaliki Wanu Wogaŵila Magazini UMOYO WATHU WACIKRISTU Landilani Alendo March 14-20 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOBU 1-5 Yobu Anakhalabe Wokhulupilika Pamene Anali Kuyesedwa March 21-27 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOBU 6-10 Munthu Wokhulupilika Yobu Afotokoza Mavuto Ake March 28–April 3 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOBU 11-15 Yobu Anali ndi Cikhulupililo Cakuti Akufa Adzauka UMOYO WATHU WACIKRISTU Ciukililo Cidzatheka Kupitila mu Nsembe ya Dipo