November Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano November 2017 Maulaliki a Citsanzo November 6-12 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | AMOSI 1-9 Funani-funani Yehova, Kuti Mukhalebe na Moyo UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kupanga Ulendo Wobwelelako November 13-19 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | OBADIYA 1–YONA 4 Tizitengelapo Phunzilo pa Zolakwa Zathu CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU Zimene Tiphunzilamo m’Buku la Yona November 20-26 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MIKA 1-7 Kodi Yehova Amafunanji kwa Ise? November 27–December 3 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | NAHUMU 1–HABAKUKU 3 Khalanibe Achelu ndi Okangalika Kuuzimu UMOYO WATHU WACIKHRISTU Khalanibe Achelu ndi Okangalika Zinthu Zikasintha mu Umoyo Wanu