March Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano March 2018 Makambilano Acitsanzo March 5-11 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MATEYU 20-21 “Aliyense Wofuna Kukhala Wamkulu Pakati Panu Ayenela Kukhala Mtumiki Wanu” March 12-18 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU MATEYU 22-23 Muzitsatila Malamulo Aŵili Aakulu a m’Cilamulo UMOYO WATHU WACIKHRISTU Tingacite Ciani Kuti Tikulitse Cikondi Cathu kwa Mulungu na kwa Mnansi Wathu? March 19-25 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MATEYU 24 Khalanibe Ogalamuka m’Masiku Otsiliza Ano UMOYO WATHU WACIKHRISTU Tili ku Mapeto a Dongosolo Lino la Zinthu March 26–April 1 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MATEYU 25 “Khalanibe Maso” UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kunola Luso Lathu mu Ulaliki Kuthandiza Maphunzilo Athu a Baibo Kukonzekela