LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 September tsa. 5
  • Sipanawonongeke Ciliconse

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Sipanawonongeke Ciliconse
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Khalani Mmisili Waluso
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Pitilizani Kuonetsa Kukula kwa Cikondi Canu Pa Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Cigawo 1
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Mungamutumikile Yehova Ngakhale Kuti Makolo anu Sanapeleke Citsanzo Cabwino
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 September tsa. 5
Likulu lathu ku Warwick, mu mzinda wa New York

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Sipanawonongeke Ciliconse

Yesu atadyetsa mozizwitsa amuna 5,000 kuphatikizapo azimayi na ŵana, anauza ophunzila ake kuti: “Sonkhanitsani zotsala zonse, kuti pasawonongeke ciliconse.” (Yoh. 6:12) Yesu anaonetsa kuyamikila pa zimene Yehova anawapatsa mwa kusawononga ciliconse.

Masiku ano, Bungwe Lolamulila limayesetsa kutengela citsanzo ca Yesu mwa kuseŵenzetsa bwino zopeleka zaufulu. Mwacitsanzo, pomanga likulu lathu ku Warwick, mu mzinda wa New York, abale anasankha pulani ya kamangidwe yosawonongetsa kwambili zopeleka zaufulu.

TINGAPEWE BWANJI KUKHALA WOWONONGA . . .

  • M’bale azima malaiti pa Nyumba ya Ufumu

    pamene tili pa misonkhano?

  • Wa Mboni za Yehova alemba dzina lake m’Baibo yake

    potenga zofalitsa zathu zokaŵelenga? (km 5/09 peji 3 pala. 4)

  • M’bale atenga tumapepa tokha tumene afuna kukagaŵila

    potenga zofalitsa zokagaŵila mu ulaliki? (mwb17.02 peji 4 pala. 1)

  • Asanapatse mzimayi buku lililonse, mlongo afuna kudziŵa ngati mzimayiyo alidi na cidwi.

    pamene tili mu ulaliki? (mwb17.02 peji 4 pala. 2, na bokosi)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani