LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 13
  • Yehova Amasintha Cizunzo Kukhala Njila Yocitila Umboni

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Amasintha Cizunzo Kukhala Njila Yocitila Umboni
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mukhoza Kupilila Pamene Mukuzunzidwa
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Kondwelani Pamene Mukuzunzidwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Khalani Ololela Potengela Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 13

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Yehova Amasintha Cizunzo Kukhala Njila Yocitila Umboni

Nthawi zambili anthu amatizunza na colinga cakuti tileke kugwila nchito yolalikila. Koma kukhulupilika kwathu tikamazunzidwa kumacitila umboni wamphamvu.

PENYELELALI VIDIYO YAKUTI KUFUNSA MAFUNSO M’BALE DMITRIY MIKHAYLOV, NDIYENO YANKHANI MAFUNSO AYA:

  • Mbali ya vidiyo yakuti ‘Kufunsa Mafunso M’bale Dmitriy Mikhaylov.’ M’bale Dmitriy watengedwa na apolisi aŵili atamumanga mu unyolo.

    Kodi M’bale Mikhaylov anakumana na cizunzo cotani?

  • Mbali ya vidiyo yakuti ‘Kufunsa Mafunso M’bale Dmitriy Mikhaylov.’ Dmitriy alemba kalata ali m’ndende. Makalata ocokela kwa mkazi wake ali pathebulo.

    Kodi Yehova anamuthandiza bwanji M’bale Mikhaylov kupilila?

  • Kodi Yehova anaseŵenzetsa bwanji cizunzo ca M’bale Mikhaylov pocitila umboni kwa akaidi ena?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani