Nowa na banja lake akukonzekela kuloŵa m’cingalawa
Makambilano Acitsanzo
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi dzina la Mulungu n’ndani?
Lemba: Sal. 83:18
Ulalo: Kodi khalidwe lalikulu la Yehova ni liti?
○●○ ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA
Funso: Kodi khalidwe lalikulu la Yehova ni liti?
Lemba: 1 Yoh. 4:8
Ulalo: Mungacite ciani kuti mukhale bwenzi la Mulungu?
○○● ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI
Funso: Mungacite ciani kuti mukhale bwenzi la Mulungu?
Lemba: Yoh. 17:3
Ulalo: Kodi Yehova amatiuza zimene zidzacitika kutsogolo?