-
Numeri 27:18-20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Tenga Yoswa mwana wa Nuni, munthu wolimba mtima,* ndipo uike dzanja lako pa iye.+ 19 Kenako umuimiritse pamaso pa wansembe Eleazara komanso pamaso pa gulu lonse, ndipo umuike kuti akhale mtsogoleri pamaso pawo.+ 20 Umupatseko mphamvu zako,*+ kuti gulu lonse la Aisiraeli lizimumvera.+
-