Numeri 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako Yoswa+ mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+ Numeri 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Numeri 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Nonsenu simudzalowa mʼdziko limene ndinalumbira* kuti mudzakhalamo,+ kupatula Kalebe mwana wa Yefune ndi Yoswa mwana wa Nuni.+ Numeri 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Amuna amene akakugawireni malo kuti akhale cholowa chanu, mayina awo ndi awa: Wansembe Eleazara+ ndi Yoswa+ mwana wa Nuni.
28 Kenako Yoswa+ mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+
30 Nonsenu simudzalowa mʼdziko limene ndinalumbira* kuti mudzakhalamo,+ kupatula Kalebe mwana wa Yefune ndi Yoswa mwana wa Nuni.+
17 “Amuna amene akakugawireni malo kuti akhale cholowa chanu, mayina awo ndi awa: Wansembe Eleazara+ ndi Yoswa+ mwana wa Nuni.