Yobu 30:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma pano amandinyoza ngakhale akamaimba nyimbo zawo,+Ndakhala chinthu choseketsa* kwa iwo.+ 10 Amanyansidwa nane ndipo safuna kundiyandikira.+Sazengereza kundilavulira kumaso.+
9 Koma pano amandinyoza ngakhale akamaimba nyimbo zawo,+Ndakhala chinthu choseketsa* kwa iwo.+ 10 Amanyansidwa nane ndipo safuna kundiyandikira.+Sazengereza kundilavulira kumaso.+