Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 49:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene angathe kuwombola mʼbale wake,

      Kapena kumuperekera dipo kwa Mulungu,+

  • Salimo 49:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Kuti akhale ndi moyo mpaka kalekale osaona dzenje la manda.+

  • Salimo 143:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ndiyankheni mofulumira, inu Yehova.+

      Mphamvu zanga zatha.*+

      Musandibisire nkhope yanu,+

      Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani