Salimo 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandiiwala?+ Kodi ndiziyenda wachisoni chifukwa chiyani? Nʼchifukwa chiyani adani anga akundipondereza?”+ Salimo 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+ Nʼchifukwa chiyani mwanditaya? Kodi ndiziyenda wachisoni chifukwa chiyani? Nʼchifukwa chiyani adani anga akundipondereza?+
9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandiiwala?+ Kodi ndiziyenda wachisoni chifukwa chiyani? Nʼchifukwa chiyani adani anga akundipondereza?”+
2 Inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+ Nʼchifukwa chiyani mwanditaya? Kodi ndiziyenda wachisoni chifukwa chiyani? Nʼchifukwa chiyani adani anga akundipondereza?+