Salimo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzaweruza anthu okhala padziko lapansi mwachilungamo.+Adzapereka zigamulo zolungama pa milandu ya mitundu ya anthu.+ Salimo 96:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Lengezani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala Mfumu.+ Dziko lapansi lakhazikika moti silingasunthidwe.* Iye adzaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo.”*+ Salimo 98:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Aroma 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
8 Iye adzaweruza anthu okhala padziko lapansi mwachilungamo.+Adzapereka zigamulo zolungama pa milandu ya mitundu ya anthu.+
10 Lengezani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala Mfumu.+ Dziko lapansi lakhazikika moti silingasunthidwe.* Iye adzaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo.”*+