Salimo 67:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mitundu ya anthu isangalale ndi kufuula mokondwera,+Chifukwa inu mudzaweruza anthu mwachilungamo.+ Mudzatsogolera mitundu ya anthu padziko lapansi. (Selah) Salimo 98:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
4 Mitundu ya anthu isangalale ndi kufuula mokondwera,+Chifukwa inu mudzaweruza anthu mwachilungamo.+ Mudzatsogolera mitundu ya anthu padziko lapansi. (Selah)