1 Mbiri 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 96:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Lengezani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala Mfumu.+ Dziko lapansi lakhazikika moti silingasunthidwe.* Iye adzaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo.”*+ Salimo 97:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Yehova wakhala Mfumu!+ Dziko lapansi lisangalale.+ Zilumba zambiri zikondwere.+ Chivumbulutso 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
10 Lengezani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala Mfumu.+ Dziko lapansi lakhazikika moti silingasunthidwe.* Iye adzaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo.”*+