Nyimbo ya Solomo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu ana aakazi a ku Yerusalemu, ine ndine wakuda koma wokongola,Ngati matenti a ku Kedara+ komanso nsalu za matenti+ a Solomo. Nyimbo ya Solomo 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘Kodi mkazi amene akuwala* ngati mʼbandakuchayu ndi ndani,Amene ndi wokongola ngati mwezi wathunthu,Wosadetsedwa ngati kuwala kwa dzuwa,Wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera?’”+
5 Inu ana aakazi a ku Yerusalemu, ine ndine wakuda koma wokongola,Ngati matenti a ku Kedara+ komanso nsalu za matenti+ a Solomo.
10 ‘Kodi mkazi amene akuwala* ngati mʼbandakuchayu ndi ndani,Amene ndi wokongola ngati mwezi wathunthu,Wosadetsedwa ngati kuwala kwa dzuwa,Wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera?’”+