-
Nyimbo ya Solomo 1:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 “Ndiwe wokongola wokondedwa wanga.
Ndiwe chiphadzuwa. Maso ako ali ngati maso a njiwa.”+
-
-
Nyimbo ya Solomo 4:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Watenga mtima wanga,+ iwe mchemwali wanga, mkwatibwi wanga,
Watenga mtima wanga utangondiyangʼana kamodzi kokha,
Ndiponso ndi mkanda wa mʼkhosi mwako.
-