Nyimbo ya Solomo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yangʼana kumbali kuti maso ako+ asandiyangʼanitsitse,Chifukwa akundichititsa mantha. Tsitsi lako lili ngati gulu la mbuziZimene zikuthamanga potsika mapiri a ku Giliyadi.+
5 Yangʼana kumbali kuti maso ako+ asandiyangʼanitsitse,Chifukwa akundichititsa mantha. Tsitsi lako lili ngati gulu la mbuziZimene zikuthamanga potsika mapiri a ku Giliyadi.+