-
Yesaya 3:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Tamverani! Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,
Akuchotsa mu Yerusalemu ndi mu Yuda zinthu zonse zofunika pa moyo,
Monga mkate ndi madzi.+
-
Maliro 4:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Amene anaphedwa ndi lupanga aliko bwino kusiyana ndi amene anafa ndi njala.+
Amenewa anafooka nʼkufa chifukwa chosowa chakudya ndipo anafa ngati abayidwa ndi lupanga.
-
-
-