-
Ezekieli 23:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Wamkulu dzina lake anali Ohola,* wamngʼono anali Oholiba.* Akazi amenewa anakhala anga ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi. Ohola akuimira Samariya+ ndipo Oholiba akuimira Yerusalemu.
5 Ohola anayamba kuchita uhule+ ngakhale kuti anali mkazi wanga. Ankalakalaka kugona ndi amuna amene ankamukonda kwambiri+ omwe ndi Asuri amene ankakhala moyandikana naye.+
-
-
Hoseya 4:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Anthu anga amafunsira kwa mafano awo amtengo,
Ndipo amachita zimene ndodo yawo* yawauza.
Chifukwa chakuti mtima wachiwerewere umawasocheretsa,
Ndiponso chifukwa cha chiwerewere chawocho, amakana kugonjera Mulungu wawo.
-