DEUTERONOMO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Kuchoka paphiri la Horebe (1-8)
Anasankha atsogoleri komanso oweruza (9-18)
Anthu sanamvere ku Kadesi-barinea (19-46)
2
3
Anagonjetsa Mfumu Ogi ya ku Basana (1-7)
Malire a dziko kumʼmawa kwa mtsinje wa Yorodano (8-20)
Yoswa anauzidwa kuti asachite mantha (21, 22)
Mose sadzalowa mʼdziko (23-29)
4
Anawalimbikitsa kuti akhale omvera (1-14)
Yehova amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha (15-31)
Palibe Mulungu wina kupatulapo Yehova (32-40)
Mizinda yothawirako kumʼmawa kwa Yorodano (41-43)
Anawapatsa Chilamulo (44-49)
5
Yehova anachita pangano ku Horebe (1-5)
Anabwereza kuwauza Malamulo Khumi (6-22)
Anthu anachita mantha paphiri la Sinai (23-33)
6
Muzikonda Yehova ndi mtima wanu wonse (1-9)
Musaiwale Yehova (10-15)
Musamamuyese Yehova (16-19)
Mudzafotokozere mʼbadwo wotsatira (20-25)
7
Mitundu 7 yoyenera kuwonongedwa (1-6)
Chifukwa chimene anasankhira Aisiraeli (7-11)
Kumvera kumabweretsa madalitso (12-26)
8
9
10
11
Mwaona mphamvu za Yehova (1-7)
Dziko Lolonjezedwa (8-12)
Madalitso amene adzapeze chifukwa chomvera (13-17)
Muzisunga mawu a Mulungu mʼmitima yanu (18-25)
“Dalitso ndi temberero” (26-32)
12
Muzilambira pamalo amene Mulungu anasankha (1-14)
Analoledwa kudya nyama koma osati magazi (15-28)
Musagwidwe mʼmisampha ya milungu ina (29-32)
13
14
Zinthu zosayenera kuchita polira maliro (1, 2)
Zakudya zodetsedwa komanso zosadetsedwa (3-21)
Chakhumi choperekedwa kwa Yehova (22-29)
15
Ankakhululukira angongole chaka cha 7 chilichonse (1-6)
Kuthandiza osauka (7-11)
Akapolo ankamasulidwa chaka cha 7 chilichonse (12-18)
Nyama zoyamba kubadwa zinali zopatulika (19-23)
16
Pasika; Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa (1-8)
Chikondwerero cha Masabata (9-12)
Chikondwerero cha Misasa (13-17)
Kusankha oweruza (18-20)
Zinthu zosayenera kuzilambira (21, 22)
17
Nsembe zizikhala zopanda chilema (1)
Zoyenera kuchita ndi ampatuko (2-7)
Milandu yovuta kuweruza (8-13)
Malangizo oti mafumu azidzatsatira (14-20)
18
Zimene ansembe ndi Alevi ankayenera kulandira (1-8)
Anawaletsa kuchita zamizimu (9-14)
Mneneri ngati Mose (15-19)
Mmene tingadziwire aneneri abodza (20-22)
19
Mlandu wa magazi komanso mizinda yothawirako (1-13)
Zizindikiro za malire sizinkafunika kusunthidwa (14)
Anthu operekera umboni mukhoti (15-21)
20
21
Ngati wopha munthu sakudziwika (1-9)
Kukwatira akazi ogwidwa kunkhondo (10-14)
Ufulu wa mwana woyamba kubadwa (15-17)
Mwana wosamvera (18-21)
Munthu wopachikidwa pamtengo ndi wotembereredwa (22, 23)
22
Kulemekeza ziweto za anthu ena (1-4)
Kuvala zovala zachimuna kapena zachikazi (5)
Kuchitira chifundo ziweto (6, 7)
Kampanda kapadenga la nyumba (8)
Zinthu zosayenera kuphatikizidwa (9-11)
Ulusi wa mʼmphepete mwa zovala (12)
Malamulo a milandu yokhudza kugonana (13-30)
23
Anthu osayenera kulowa mumpingo wa Mulungu (1-8)
Ukhondo mumsasa (9-14)
Kapolo amene wathawa kwa mbuye wake (15, 16)
Uhule unaletsedwa (17, 18)
Chiwongoladzanja komanso malonjezo (19-23)
Zimene anthu ongodutsa ankaloledwa kudya (24, 25)
24
Ukwati komanso kutha kwa ukwati (1-5)
Kulemekeza moyo (6-9)
Kuganizira osauka (10-18)
Malamulo okhudza kukunkha (19-22)
25
Malamulo okhudza kukwapula munthu (1-3)
Ngʼombe imene ikupuntha mbewu musamaimange pakamwa (4)
Ukwati wapachilamu (5-10)
Kugwira malo osayenera pandewu (11, 12)
Muyezo woyenera woyezera kulemera komanso kuchuluka kwa zinthu (13-16)
Aamaleki ayenera kuwonongedwa (17-19)
26
Kupereka zipatso zoyambirira (1-11)
Chakhumi chachiwiri (12-15)
Aisiraeli anali chuma chapadera kwa Yehova (16-19)
27
Akalembe Chilamulo pamiyala (1-10)
Paphiri la Ebala ndi paphiri la Gerizimu (11-14)
Anatchulanso matemberero (15-26)
28
29
30
Kubwerera kwa Yehova (1-10)
Malamulo a Yehova si ovuta kwambiri (11-14)
Kusankha moyo kapena imfa (15-20)
31
Mose anali atatsala pangʼono kumwalira (1-8)
Kuwerenga Chilamulo pamaso pa anthu (9-13)
Yoswa anamuika kuti akhale mtsogoleri (14, 15)
Ananeneratu kuti Aisiraeli adzapandukira Mulungu (16-30)
32
33
34