Zimene Zili M’bukuli
MUTU TSAMBA
NKHANI YOYAMBA
1. “Pitani Mukaphunzitse Anthu . . . Kuti Akhale Ophunzira Anga” 6
GAWO 1—“Mwadzaza Yerusalemu Yense ndi Mfundo Zimene Mukuphunzitsa”
2. “Mudzakhala Mboni Zanga” 14
3. “Anadzazidwa ndi Mzimu Woyera” 21
4. “Osaphunzira Ndiponso Anthu Wamba” 28
5. “Ife Tiyenera Kumvera Mulungu Monga Wolamulira” 37
GAWO 2—“Mpingo Umene Unali ku Yerusalemu Unayamba Kuzunzidwa Koopsa”
6. “Sitefano Anali ndi Mphamvu Ndipo Ankachita Kuonekeratu Kuti Mulungu Ali Naye” 45
7. Kulalikira “Uthenga Wabwino Wonena za Yesu” 52
8. Mpingo “Unayamba Kukhala Pamtendere” 60
GAWO 3—‘Anthu a Mitundu Ina Analandira Mawu a Mulungu’
10. “Mawu a Yehova Anapitiriza Kufalikira” 77
GAWO 4—“Anatumizidwa ndi Mzimu Woyera”
11. “Anapitiriza Kukhala Osangalala Komanso Mzimu Woyera Unkawathandiza Kwambiri” 85
12. “Ankalankhula Molimba Mtima Chifukwa cha Mphamvu ya Yehova” 93
GAWO 5—“Atumwi ndi Akulu Anasonkhana”
GAWO 6—“Tiyeni Tibwerere . . . Kuti Tikachezere Abale”
15. “Ankalimbikitsa Mipingo” 117
16. “Wolokerani ku Makedoniya Kuno” 125
17. “Anakambirana Nawo Mfundo za M’Malemba” 133
18. ‘Funafunani Mulungu ndi Kumupezadi’ 140
19. ‘Pitiriza Kulankhula, Usakhale Chete’ 148
GAWO 7—‘Ankaphunzitsa Pagulu Komanso Kunyumba ndi Nyumba’
20. “Anapitiriza Kufalikira Ndipo Sankagonjetseka” Ngakhale Kuti Panali Otsutsa 157
21. “Ndilibe Mlandu wa Magazi a Anthu Onse” 165
22. “Chifuniro cha Yehova Chichitike” 173
GAWO 8—“Ankawalalikira za Ufumu wa Mulungu . . . Popanda Choletsa”
23. “Mvetserani Mawu Anga Odziteteza” 181
25. “Ndikuchita Apilo Kuti Ndikaonekere kwa Kaisara” 196
26. “Palibe Amene Ataye Moyo Wake” 203
27. “Anachitira Umboni Mokwanira” 211