July 27–August 2
EKISODO 12
Nyimbo Na. 20 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kufunika kwa Mwambo wa Pasika kwa Akhristu”: (10 min.)
Eks 12:5-7—Kufunika kwa mwana wa nkhosa wa pa Pasika (w07 1/1 20 ¶4)
Eks 12:12, 13—Kufunika kwa magazi omwe anapakidwa pamafelemu a zitseko (it-2 583 ¶6)
Eks 12:24-27—Zimene tingaphunzire kuchokera pa zomwe zinkachitika pa mwambo wa Pasika (w13 12/15 20 ¶13-14)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Eks 12:12—N’chifukwa chiyani miliri imene inagwera Aiguputo, makamaka wa 10, kunali kuweruza milungu yawo yonyenga? (it-2 582 ¶2)
Eks 12:14-16—Mofanana ndi misonkhano ina yopatulika, kodi Chikondwerero cha Mikate Yopanda Chofufumitsa chinali chapadera m’njira iti, nanga chinkathandiza bwanji Aisiraeli? (it-1 504 ¶1)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks 12:1-10 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 2)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni magazini yaposachedwapa yomwe ili ndi nkhani yomwe mwakambirana. (th phunziro 6)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 16 ¶21-22 (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Yehova Amateteza Anthu Ake”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kuona Malo Osungirako Zinthu Zakale ku Warwick: “Anthu Odziwika ndi Dzina la Yehova”.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia 6:9-18
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 41 ndi Pemphero