CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | DANIELI 7-9
Ulosi wa Danieli Unaneneratu Nthawi Imene Mesiya Adzafike
zosindikizidwa
“MILUNGU 70” (ZAKA 490)
“MILUNGU 7” (ZAKA 49)
455 B.C.E. “Mawu . . . onena kuti Yerusalemu akonzedwe”
406 B.C.E. Yerusalemu anamangidwanso
“MILUNGU 62” (ZAKA 434)
“MLUNGU UMODZI” (ZAKA 7)
29 C.E. Mesiya anafika
33 C.E. Mesiya ‘anaphedwa’
36 C.E. Mapeto a “milungu 70”