Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.05 7
  • Pewani Msampha Woopa Anthu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Pewani Msampha Woopa Anthu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • “Ndakupatsani Chitsanzo”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • “Simuli Mbali ya Dzikoli”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • N’zotheka Kupirira Ena Akamakuzunzani
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • “Osaphunzira Ndiponso Anthu Wamba”
    ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.05 7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALIKO 13-14

Pewani Msampha Woopa Anthu

N’chifukwa chiyani atumwi anakodwa mumsampha woopa anthu?

14:29, 31

  • Ankadzidalira kwambiri. Mwachitsanzo Petulo ankaona kuti iyeyo adzakhalabe wokhulupirika kwa Yesu kuposa atumwi enawo

    Petulo akukana Yesu

14:32, 37-41

  • Iwo analephera kukhalabe maso komanso anasiya kupemphera

    Atumwi akugona pamene Yesu akupemphera

Yesu ataukitsidwa, n’chiyani chinathandiza atumwi kuti asamaope anthu n’kumalalikirabe ngakhale kuti ankatsutsidwa?

13:9-13

  • Anamvera machenjezo a Yesu ndipo zotsatira zake analimba mtima pamene ankatsutsidwa komanso kuzunzidwa

  • Anadalira Yehova komanso anapemphera.​—Mac. 4:24, 29

    Petulo ndi Yohane ali m’bwalo la Sanihedirini

Kodi ndi zochitika ziti zimene zingachititse kuti kulimba mtima kukhale kovuta?

Mayi wa Mboni ali m’chipatala ndipo akukambirana ndi dokotala; mnyamata wa Mboni ali m’kalasi ndipo sakuchitira nawo saluti mbendera; wa Mboni akulandira khadi yomuitanira kuphwando la kuntchito
    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani