Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.10 5
  • “Ndakupatsani Chitsanzo”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Ndakupatsani Chitsanzo”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Amaona Kuti Atumiki Ake Odzichepetsa Ndi Amtengo Wapatali
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
  • Pewani Msampha Woopa Anthu
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • “Chilimikani ndi Kuona Chipulumutso cha Yehova”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.10 5
Yesu akusambitsa mapazi a atumwi ake

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 13-14

“Ndakupatsani Chitsanzo”

13:5, 12-15

Pamene Yesu anasambitsa mapazi a ophunzira ake, anawaphunzitsa kuti akhale odzichepetsa komanso azigwira ntchito zooneka zotsika pothandiza abale awo.

Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndine wodzichepetsa . . .

  • Alongo awiri asemphana maganizo

    ndikasemphana maganizo ndi anthu ena?

  • M’bale wina akupereka malangizo kwa mnzake

    ena akandipatsa malangizo?

  • Abale ndi alongo akugwira ntchito yoyeretsa pa Nyumba ya Ufumu

    ndikamagwira nawo ntchito yosamalira kapena kukonza Nyumba ya Ufumu?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani