Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.07 4
  • Fanizo la Msamariya Wachifundo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Fanizo la Msamariya Wachifundo
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Fanizo la Mwana Wolowerera
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Zomwe Tikuphunzira M’fanizo la Ndalama 10 za Mina
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.07 4
Msamariya wachifundo akumanga mabala a Myuda yemwe wavulazidwa

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 10-11

Fanizo la Msamariya Wachifundo

10:25-37

Yesu ananena fanizoli pamene ankayankha funso lakuti, “Nanga mnzanga amene ndikuyenera kumukonda ndani kwenikweni?” (Luka 10:25-29) Iye ankadziwa kuti mpingo wachikhristu udzapangidwa ndi anthu “osiyanasiyana” kuphatikizapo Asamariya komanso anthu a mitundu ina. (Yoh. 12:32) Fanizoli linathandiza otsatira ake kuti aziyesetsa kuchita zonse zomwe angathe kuti azikonda ena, ngakhale omwe amasiyana nawo m’zinthu zambiri.

Anthu a mitundu yosiyanasiyana akusangalalira limodzi

DZIFUNSENI KUTI:

  • ‘Kodi ndimawaona bwanji abale ndi alongo a zikhalidwe zina?’

  • ‘Kodi ndimakonda kucheza ndi anthu okhawo omwe ndimafanana nawo m’zinthu zambiri?’

  • ‘Kodi pali zimene ndingachite kuti ndidziwane bwino ndi Akhristu ochokera m’mayiko ena komanso zikhalidwe zosiyanasiyana?’ (2 Akor. 6:13)

Kod ndi ndani amene ndikufuna kuti . . .

  • adzalowe nane mu utumiki?

  • abwere kudzadya kunyumba kwathu?

  • abwere kwathu kudzachita nawo Kulambira kwa Pabanja?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani