Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.07 6
  • Fanizo la Mwana Wolowerera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Fanizo la Mwana Wolowerera
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Fanizo la Msamariya Wachifundo
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Muzikhala Okonzeka Kukhululuka
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Zomwe Tikuphunzira M’fanizo la Ndalama 10 za Mina
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Kodi Mumamvera Machenjezo?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.07 6
Mwana wolowerera akubwereranso pakhomo ndipo bambo ake akumulandira

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 14-16

Fanizo la Mwana Wolowerera

15:11-32

Mfundo zina zimene tikuphunzira mufanizoli

  • Ndi nzeru kukhalabe m’gulu la anthu a Mulungu lomwe ndi lotetezeka kwambiri komanso limene Yehova amaligwiritsa ntchito potisamalira mwachikondi

  • Ngati tayamba kuchoka panjira ya Mulungu tiyenera kudzichepetsa n’kubwerera kwa Yehova yemwe ndi wokonzeka kutikhululukira

  • Tiyenera kutengera chitsanzo cha Yehova pokhululukira komanso kulandira ndi manja awiri anthu amene abwerera mumpingo

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani