CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AGALATIYA 1-3
“Ndinamutsutsa Pamasom’pamaso”
Kodi nkhaniyi ingatiphunzitse chiyani pa mfundo zotsatirazi?
Kuchita zinthu molimba mtima.—w18.03 31-32 ¶16
Kuopa anthu kuli ngati msampha.—it-2 587 ¶43
Anthu a Yehova ngakhalenso omwe ali ndi udindo mumpingo ndi opanda ungwiro.—w10 6/15 17-18 ¶12
Timafunika kuchita khama kuti tichotse maganizo aliwonse a tsankho mumtima mwathu.—w18.08 9 ¶5