CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Musamaone Zinthu Zopanda Pake
Maso a Akani anamuchititsa kuti atenge zinthu zomwe sizinali zake (Yos 7:1, 20, 21; w10 4/15 20:5)
Zochita za Akani zinakhudza banja lake komanso mtundu wonse wa Aisiraeli (Yos 7:4, 5, 24-26; w97 8/15 28:2)
Tizikhala odziletsa (1Yo 2:15-17; w10 4/15 21:8)
Tizipewa zinthu zopanda pake zimene sizidzapezeka m’dziko latsopano lomwe mudzakhale chilungamo.—2Pe 3:13.