CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Zimene Adani Athu Amachita Pofuna Kutifooketsa
Adani athu amanena zinthu zabodza zokhudza amene akutitsogolera n’cholinga choti atifooketse (2Mf 18:19-21; w05-CN 8/1 11:5)
Amanena zabodza zokhudza Yehova kapena gulu lathu pofuna kutisocheretsa (2Mf 18:22, 25; w10-CN 7/15 13:3)
Amatinyengerera kuti tisamamvere Yehova potilonjeza zinthu zabodza (2Mf 18:31, 32; w13-CN 11/15 19:14; yb74 177:1)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingachite zotani panopa kuti ndidzathe kupirira ndikamadzazunzidwa?’