Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.05 10
  • Thawirani kwa Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Thawirani kwa Yehova
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Amaona Kuti Moyo wa Munthu Ndi Wamtengo Wapatali
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Kodi Mumathawira kwa Yehova?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • “Nyamulani Mwana Wanu”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.05 10

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Thawirani kwa Yehova

Mu Isiraeli munali mizinda 6 yoti amene wapha munthu mwangozi azithawirako (Nu 35:15; w17.11 2:4)

Akulu a mu Isiraeli ankaweruza mlandu uliwonse (Nu 35:24; w17.11 2:6)

Mizinda yothawirako inali malo achitetezo (Nu 35:25; w17.11 2:13)

Mofanana ndi munthu yemwe wapha mnzake mwangozi amene ankafunika kusiya moyo umene anazolowera kuti akhale ndi mwayi wotetezedwa ndi mizinda yothawirako, ifenso timafunika kusiya zinthu zina kuti Yehova atichitire chifundo n’kutikhululukira.

Wachinyamata wawerama ndipo akudzimvera chisoni. Zithunzi zosonyeza anthu omwe akufuna kuti Yehova awakhululukire: 1. Wochimwa yemwe walapa akufotokoza mlandu wake kwa akulu a mzinda wothawirako. 2.Wachinyamata wolapa yemwe amadzimvera chisoni uja akukumana ndi akulu awiri.
    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani