Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb22.09 23
  • “Nyamulani Mwana Wanu”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Nyamulani Mwana Wanu”
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • “Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Thawirani kwa Yehova
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Pemphero Linachititsa Yehova Kuchitapo Kanthu
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22.09 23
Mkazi wa ku Sunemu akukumbatira mosangalala mwana wake amene waukitsidwa ndipo Elisa akuonerera.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Nyamulani Mwana Wanu”

Mkazi wa ku Sunemu anachereza bwino kwambiri Elisa (2Mf 4:8-10)

Yehova anamudalitsa mayiyu ndipo anabereka mwana wamwamuna (2Mf 4:16, 17; w17.12 1:7)

Yehova anagwiritsa ntchito Elisa kuti aukitse mwanayo (2Mf 4:32-37; w17.12 1:8)

Kodi muli ndi chisoni chifukwa cha imfa ya mwana wanu? Yehova akumvetsa mmene mukumvera. Ndipo posachedwapa amuukitsa. (Yob 14:14, 15) Imeneyitu idzakhala nthawi yosangalatsa kwambiri.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani