Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.07 23
  • Kukhala Olimba Mtima Sikovuta Kwambiri

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kukhala Olimba Mtima Sikovuta Kwambiri
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • ‘Limba Mtima Ndipo Ugwire Ntchitoyi’
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • Limbani Mtima Pamene Mapeto Akuyandikira
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.07 23
Mlongo akulalikira mnzake wa kusukulu molimba mtima pogwiritsa ntchito foni.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kukhala Olimba Mtima Sikovuta Kwambiri

Munthu wolimba mtima amakhala wamphamvu komanso saopa. Koma izi sizikutanthauza kuti iye sakhaliratu wopanda mantha. M’malomwake, zikutanthauza kuti iye amachitabe zimene akufunika kuchitazo ngakhale kuti akuchita mantha. Yehova ndi amene amatithandiza kukhala olimba mtima. (Sl 28:7) Kodi achinyamata angasonyeze bwanji kulimba mtima?

ONERANI VIDIYO YAKUTI MUSAMATSANZIRE ANTHU AMANTHA, KOMA OLIMBA MTIMA, NDIPO KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi achinyamata amakumana ndi zinthu ziti zimene zimafunika kulimba mtima?

  • Kodi ndi nkhani za m’Baibulo ziti zimene zingatithandize kukhala olimba mtima?

  • Kodi kulimba mtima kumathandiza bwanji ifeyo komanso anthu ena omwe akutiona?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani