Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.11 20
  • Kudzichepetsa N’kwabwino Osati Kunyada

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kudzichepetsa N’kwabwino Osati Kunyada
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • “Pita ndi Mphamvu Zimene Ndakupatsazi”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Amaona Kuti Atumiki Ake Odzichepetsa Ndi Amtengo Wapatali
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
  • Musamadziganizire Kuposa Mmene Muyenera Kudziganizira
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2020
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.11 20

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kudzichepetsa N’kwabwino Osati Kunyada

Kudzichepetsa kunathandiza Gidiyoni kukhazikitsa mtendere (Owe 8:1-3; w00 8/15 25 ¶3)

Chifukwa choti Gidiyoni anali wodzichepetsa, ankafuna kuti anthu azitamanda Yehova osati iyeyo (Owe 8:22, 23; w17.01 20 ¶15)

Kunyada kunachititsa kuti Abimeleki komanso anthu ena awonongedwe (Owe 9:1, 2, 5, 22-24; w08 2/15 9 ¶9)

Mwininyumba wolusa akukalipira banja lomwe likufuna kumulalikira.

Kodi kudzichepetsa kungatithandize bwanji tikakumana ndi mwininyumba wolusa?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani