Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb22.03 20
  • Kodi Mumachita Zinthu Mopupuluma?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mumachita Zinthu Mopupuluma?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Muzimuuza Yehova Zamumtima Mwanu Mukamapemphera
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Anachita Zinthu Mwanzeru
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • “Kodi Mukayikakayika Mpaka Liti?”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22.03 20
Zithunzi: 1. Davide akuimitsa amuna omwe ali ndi zida amene anali naye pamene akumana ndi Abigayeli ndi atumiki ake omwe anyamula chakudya. 2. Modzichepetsa, Abigayeli wagwada pamaso pa Davide pomuchonderera.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mumachita Zinthu Mopupuluma?

Davide anapempha zinthu mwaulemu koma anayankhidwa mwachipongwe (1Sa 25:7-11; ia 9:10-12)

Davide ankafuna kupha amuna onse a m’nyumba ya Nabala (1Sa 25:13, 21, 22)

Abigayeli anathandiza Davide kuti asapalamule mlandu wa magazi (1Sa 25:25, 26, 32, 33; ia 9:18)

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ndimachita zinthu mopupuluma ndikakwiya, ndikamagula zinthu, kapena ndikafooka? Kapena kodi ndimayamba ndaganiza kaye zomwe zingatsatirepo?’​—Miy 15:28; 22:3.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani