Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb22.09 16
  • Tizidalira Yehova Kuti Atilimbikitse

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tizidalira Yehova Kuti Atilimbikitse
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • “Kodi Mukayikakayika Mpaka Liti?”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • B8 Kachisi Amene Solomo Anamanga
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Kodi Mumachita Zinthu Mopupuluma?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22.09 16

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tizidalira Yehova Kuti Atilimbikitse

Eliya anachita mantha ndipo anathawa kuti apulumutse moyo wake (1Mf 19:3, 4; w19.06 25:5)

Yehova anamuthandiza Eliya ndipo anamusonyeza mphamvu zake m’njira zodabwitsa kwambiri (1Mf 19:5-7, 11, 12; ia 12:13; 12:21)

Yehova anamupatsa ntchito yoti agwire (1Mf 19:15-18; ia 12:22)

M’bale amene wamangidwa akulalikira kwa woyang’anira ndende.

Masiku ano, Yehova amatilankhula kudzera m’Mawu ake ndipo amatikumbutsa kuti amatikonda komanso kuti anatipatsa utumiki wofunika kwambiri woti tichite.​—1Ak 15:58; Akl 3:23.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani