Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb22.11 22
  • Muzisangalala Mukamazunzidwa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzisangalala Mukamazunzidwa
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • N’zotheka Kupirira Ena Akamakuzunzani
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Muzitsatira Mapazi a Khristu Mosamala Kwambiri
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Tizitamanda Yehova Mosangalala Poimba Nyimbo
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22.11 22
Zithunzi za muvidiyo yakuti “Tikhoza Kumasangalalabe Ngakhale Kuti . . . Tikuzunzidwa.” M’bale Konstantin Bazhenov ali m’ndende. 1. Akuwerenga Baibulo. 2. Akupemphera. 3. Akuimba nyimbo za Ufumu mokweza mawu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzisangalala Mukamazunzidwa

Akhristu amayembekezera kuti tsiku lina adzazunzidwa. (Yoh 15:20) Ngakhale kuti kuzunzidwa kumabweretsa nkhawa komanso nthawi zina n’kopweteka, n’zotheka kumasangalala uku tikupirira.​—Mt 5:10-12; 1Pe 2:19, 20.

ONERANI VIDIYO YAKUTI TIKHOZA KUMASANGALALABE NGAKHALE KUTI TIKUZUNZIDWA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

Kodi mwaphunzira chiyani kwa M’bale Bazhenov pa nkhani ya

  • kuwerenga Baibulo tsiku lililonse?

  • kulola kuti abale ndi alongo azikuthandizani?a

  • kupemphera pafupipafupi?

  • kuimba nyimbo za Ufumu?

  • kuuza ena zimene timakhulupirira?

a Tikhoza kumapempherera Akhristu omwe ali m’ndende ngakhalenso powatchula mayina. Koma n’zosatheka kuti ofesi ya nthambi izitumiza kwa Akhristuwa makalata omwe abale ndi alongo amawalembera.

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani